Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 1:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

MAU a Amosi, amene anali mwa oweta ng'ombe a ku Tekoa, ndiwo amene anawaona za Israyeli masiku a Uziya mfumu ya Yuda, ndi masiku a Yerobiamu mwana wa Yoasi mfumu ya Israyeli, zitatsala zaka ziwiri cisanafike cibvomezi.

Werengani mutu wathunthu Amosi 1

Onani Amosi 1:1 nkhani