Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inati, Kodi atsalanso wina wa nyumba ya Sauli kuti ndimuonetsere cifundo ca Mulungu? Ziba nanena ndi mfumu, Aliponso mwana wa Jonatani wopunduka mapazi ace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 9

Onani 2 Samueli 9:3 nkhani