Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 7:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace tsono cikukomereni kudalitsa nyumba ya mnyamata wanu kuti ikhale pamaso panu cikhalire; pakuti Inu, Yehova Mulungu, munacinena; ndipo nyumba ya mnyamata wanu idalitsike ndi dalitso lanu ku nthawi zonse.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7

Onani 2 Samueli 7:29 nkhani