Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 7:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Davide mfumu analowa, nakhalapansi pamaso pa Yehova; nati, Ine ndine yani, Yehova Mulungu, ndi banja langa ndi ciani kuti munandifikitsa pano?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7

Onani 2 Samueli 7:18 nkhani