Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 4:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Isiboseti, mwana wa Sauli anali nao amuna awiri, ndiwo atsogoleri a magulu; wina dzina lace Baana, ndi dzina la mnzace ndiye Rekabu, ndiwo ana a Rimoni wa ku Beeroti, wa ana a Benjamini, pakuti Beeroti womwe unawerengedwa wa Benjamini;

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 4

Onani 2 Samueli 4:2 nkhani