Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 3:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Yoabu anadza kwa mfumu, nati, Mwacitanji? Taonani, Abineri anadza kwa inu, cifukwa ninji tsono munalawirana naye kuti acokedi.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:24 nkhani