Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Cabwino, ndidzapangana nawe; koma ndikuikira cinthu cimodzi, ndico kuti, sudzaona nkhope yanga, koma utsogole wabwera naye Mikala mwana wamkazi wa Sauli, pamene ubwera kudzaona nkhope yanga.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:13 nkhani