Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 24:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Arauna anayang'ana naona mfumuyo ndi anyamata ace alikubwera kwa iye; naturuka Arauna naweramira pamaso pa mfumu nkhope yace pansi.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:20 nkhani