Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 21:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ananka natenga mafupa a Sauli ndi mafupa a Jonatani mwana wace kwa anthu a ku Jabezi Gileadi amene anawaba m'khwalala la Betisani, kumene Afilisti adawapacika, tsiku lija Afilistiwo anapha Sauli ku Giliboa;

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:12 nkhani