Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 20:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Amasa sanasamalira lupanga liri m'dzanja la Yoabu; comweco iye anamgwaza nalo m'mimba; nakhuthula matumbo ace pansi, osamgwazanso; nafa iye, Ndipo Yoabu ndi Abisai mbale wace analondola Seba mwana wa Bikri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20

Onani 2 Samueli 20:10 nkhani