Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 2:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoabu anabwerera pakutsata Abineri. Ndipo pamene anasonkhanitsa pamodzi anthu onse anasowa anthu a Davide khumi ndi asanu ndi anai ndi Asaheli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:30 nkhani