Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 2:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Asaheli anapitikitsa Abineri. Ndipo m'kuthamanga kwace sanapambukira kulamanja, kapena kulamanzere, pakutsata Abineri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:19 nkhani