Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 2:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anagwirana munthu yense kugwira mutu wa mnzace, nagwaza ndi lupanga lace m'nthiti mwa mnzaceo Comweco anagwa limodzi; cifukwa cace malo aja anachedwa Dera la Mipeni la ku Gibeoni.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:16 nkhani