Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 18:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Abisalomu akali moyo adatenga nadziutsira coimiritsaco ciri m'cigwa ca mfumu; pakuti anati, Ndiribe mwana wamwamuna adzakhala cikumbutso ca dzina langa; nacha coimiritsaco ndi dzina la iye yekha; ndipo cichedwa cikumbutso ca Abisalomu, kufikira lero lomwe.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:18 nkhani