Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 17:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anyamata a Abisalomu anafika kunyumba kwa mkaziyo; nati, Ali kuti Ahimaazi ndi Jonatani? Ndipo mkaziyo ananena nao, Anaoloka kamtsinje kamadzi. Ndipo atawafunafuna, osawapeza, anabwerera kumka ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17

Onani 2 Samueli 17:20 nkhani