Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 16:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Abisai mwana wa Zeruya ananena ndi mfumu, Garu wakufa uyu atukwaniranji mbuye wanga mfumu? Mundilole ndioloke ndi kudula mutu wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 16

Onani 2 Samueli 16:9 nkhani