Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 16:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali pakudza kwa Abisalomu Husai M-ariki, bwenzi la Davide, Husai ananena ndi Abisalomu, Mfumu ikhale ndi moyo, Mfumu ikhale ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 16

Onani 2 Samueli 16:16 nkhani