Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma ukabwerera kumudzi, ndi kunena ndi Abisalomu, Ine ndine mnyamata wanu, mfumu; monga kale ndinali mnyamata wa atate wanu, momwemo tsopano ndidzakhala mnyamata wanu; pomwepo udzanditsutsira uphungu wa Ahitofeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:34 nkhani