Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 14:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pometa tsitsi lace amameta potsiriza caka, cifukwa tsitsi linamlemerera, cifukwa cace atalimeta anayesa tsitsi la pa mutu wace, napeza masekeli mazana awiri, monga mwa muyeso wa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:26 nkhani