Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 13:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Jonadabu mwana wa Simeya mbale wa Davide anayankha nati, Mbuye wanga asaganize kuti anapha anyamata onse, ana amuna a mfumu, pakuti Amnoni yekha wafa, pakuti Ici cinatsimikizika ndi mau a Abisalomu kuyambira tsiku lija anacepetsa mlongo: wace Tamara.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:32 nkhani