Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 13:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Tamara anathira phulusa pamutu pace, nang'amba cobvala ca mawanga mawanga cimene analikubvala, nagwira dzanja lace pamutu pace, namuka nayenda, nalira komveka.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:19 nkhani