Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 13:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anabvala cobvala ca mawanga mawanga, popeza ana akazi a mfumu okhala anamwali amabvala zotere. Ndipo mnyamata wace anamturutsa, napiringidza citseko atapita iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:18 nkhani