Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 13:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atatero Amnoni anadana naye ndi cidani cacikuru kopambana; pakuti cidani cimene anamuda naco, cinali cacikuru koposa cikondi adamkonda naco. Ndipo Amnoni ananena naye, Nyamuka, coka.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:15 nkhani