Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 11:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Davide ananena ndi mthengawo, Udzatero kwa Yoabu, Cisakuipire ici, lupanga limaononga ina ndi mnzace. Onjeza kulimbitsa nkhondo yako pamudzipo, nuupasule; numlimbikitse motere.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 11

Onani 2 Samueli 11:25 nkhani