Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 10:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene ana a Amoni anazindikira kuti anadzinunkhitsa kwa Davide, ana a Amoniwo anatumiza nadzilembera Aaramu a ku Betirehobu, ndi Aaramu a ku Zoba, oyenda pansi zikwi makumi awiri, ndi mfumu ya ku Maaka ndi anthu cikwi cimodzi, ndi anthu a mfumu ya ku Tobu zikwi khumi ndi ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10

Onani 2 Samueli 10:6 nkhani