Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 10:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene anaciuza Davide iye anatumiza anthu kukakomana nao; pakuti amunawo anacita manyazi akuru. Niti mfumu, Bakhalani ku Yeriko kufikira zamera ndebvuzanu; zitameramubwere.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10

Onani 2 Samueli 10:5 nkhani