Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 10:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wina anauza Davide; iye nasonkhanitsa Aisrayeli onse, naoloka Yordano nafika ku Helemu, Ndipo Aaramu anandandalitsa nkhondo yao pa Davide namenyana naye.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10

Onani 2 Samueli 10:17 nkhani