Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 1:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pa tsiku lacitatu, onani, munthu anaturuka ku zithando za Sauli, ali ndi zobvala zace zong'ambika, ndi dothi pamutu pace; ndipo kunatero kuti iye, pofika kwa Davide, anagwa pansi namgwadira.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 1

Onani 2 Samueli 1:2 nkhani