Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 1:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'mwemo ndinakhala pambali pace ndi kumtsiriza cifukwa ndinadziwa kuti sangakhalenso ndi moyo wace, atagwa. Ndipo ndinatenga korona wa pamutu pace, ndi cigwinjiri ca pa mkono wace, ndabwera nazo kuno kwa mbuye wanga.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 1

Onani 2 Samueli 1:10 nkhani