Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atatha tsono Solomo kupemphera, moto unatsika kumwamba, nunyeketsa nsembe yopsereza, ndi nsembe zophera; ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza nyumbayi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 7

Onani 2 Mbiri 7:1 nkhani