Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 6:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mverani mapembedzero a kapolo wanu ndi a anthu anu Israyeli, popemphera iwo kuloza konkuno; ndipo mumvere Inu m'Mwamba mokhala Inumo, ndipo pakumva Inu, mukhululikire.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:21 nkhani