Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 6:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti maso anu atsegukire nyumba iyi usana ndi usiku, malo amene munanenerako kuti mudzaikako dzina lanu, kuti mumvere pemphero limene kapolo wanu adzapempha kuloza konkuno.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:20 nkhani