Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 6:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Solomo anati, Yehova anati kuti adzakhala mu mdima wandiweyani.

2. Koma ndakumangirani nyumba yokhalamo, malo okhazikika okhalamo Inu nthawi yosatha.

3. Ndipo mfumu inapotolokera nkhope yace, nidalitsa khamu lonse la Israyeli; ndi khamu lonse la Israyeli linaimirira.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6