Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 6:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Alemekezedwe Yehova Mulungu wa Israyeli, wakunena m'kamwa mwace ndi Davide atate wanga, nakwaniritsa: ndi manja ace, ndi kuti,

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:4 nkhani