Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo zidatha nchito zonse Solomo adazicitira nyumba ya Yehova. Ndipo Solomo anabwera nazo zopatulika zija za atate wace Davide; naziika siliva, ndi golidi, ndi zipangizo zonse m'cuma ca nyumba ya Mulungu.Kuperekedwa kwa Kacisi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 5

Onani 2 Mbiri 5:1 nkhani