Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 4:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi zozimira nyali, ndi mbale zowazira, ndi zipande, ndi mbale za zofukiza za golidi woona; ndi kunena za polowera m'nyumba, zitseko zace za m'katimo za malo opatulikitsa, ndi zitseko za nyumbayi, ndiyo Kacisi, zinali zagolidi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 4

Onani 2 Mbiri 4:22 nkhani