Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 36:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu ya Aigupto anamcotsera ufumu wace m'Yerusalemu, nasonkhetsa dziko matalente zana limodzi a siliva, ndi talente limodzi la golidi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 36

Onani 2 Mbiri 36:3 nkhani