Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 35:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Panalibe Paskha wocitika m'Israyeli wonga ameneyu, kuyambira masiku a Samueli mneneri; panalibenso wina wa mafumu a Israyeli anacita Paskha wotere, ngati ameneyu anacita Yosiya, ndi ansembe, ndi Alevi, ndi Ayuda onse, ndi Aisrayeli opezekako, ndi okhala m'Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:18 nkhani