Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 34:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu anagumula maguwa a nsembe a Abaala pamaso pace; nawalikha mafano a dzuwa anakwezeka pamwamba pao; naphwanya zifanizo, ndi mafano osema, ndi mafano oyenga; nazipera, naziwaza pamanda pa iwo amene adaziphera nsembe.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 34

Onani 2 Mbiri 34:4 nkhani