Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 34:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Namuka Hilikiya ndi iwo aja adawauza mfumu kwa Hulida mneneri wamkazi, mkazi wa Salumu mwana wa Tokati, mwana wa Hasire wosunga zobvala, amene anakhala m'Yerusalemu m'dera laciwiri, nanena naye mwakuti.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 34

Onani 2 Mbiri 34:22 nkhani