Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 34:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amunawo anacita nchitoyi mokhulupirika; ndi oikidwa awayang'anire ndiwo Yohati ndi Obadiya, Alevi, a ana a Merari; ndi Zekariya ndi Mesulamu, a ana a Akohati, kuifulumiza; ndi Alevi ena ali yense wa luso la zoyimbira,

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 34

Onani 2 Mbiri 34:12 nkhani