Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 32:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hezekiya anagona ndi makolo ace, namuika polowerera ku manda a ana a Davide; ndi Ayuda onse ndi okhala m'Yerusalemu anamcitira ulemu pa imfa yace. Ndipo Manase mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32

Onani 2 Mbiri 32:33 nkhani