Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 31:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ana a Israyeli ndi Yuda okhala m'midzi ya Yuda, iwonso anabwera nalo limodzi la magawo khumi la ng'ombe, ndi nkhosa, ndi limodzi la magawo khumi la zinthu zopatulika, zopatulikira Yehova Mulungu wao; naziunjika miyuru miyuru,

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 31

Onani 2 Mbiri 31:6 nkhani