Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 31:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Citatha ici conse tsono, Aisrayeli onse opezekako anaturuka kumka ku midzi ya Yuda, naphwanya zoimiritsa, nalikha zifanizo, nagamula misanje ndi maguwa a nsembe m'Yuda monse, ndi m'Benjamini, m'Efraimunso, ndi m'Manase, mpaka adaziononga zonse. Pamenepo ana onse a Israyeli anabwerera, yense ku dziko lace ndi ku midzi yao.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 31

Onani 2 Mbiri 31:1 nkhani