Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 30:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti, anthu aunyinji, ndiwo ambiri a Efraimu, ndi Manase, Isakara, ndi Zebuloni, sanadziyeretsa, koma anadya Paskha mosati monga munalembedwa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 30

Onani 2 Mbiri 30:18 nkhani