Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 30:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naima m'malo mwao mwa kulongosoka kwao, monga mwa cilamulo ca Mose munthu wa Mulunguyo; ansembe anawaza mwazi, ataulandira ku dzanja la Alevi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 30

Onani 2 Mbiri 30:16 nkhani