Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova ku Yerusalemu, m'phiri la Moriya, kumene Mulungu anaonekera kwa Davide atate wace, pamalo pamene Davide anakonzeratu pa dwale la Orinani Myebusi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 3

Onani 2 Mbiri 3:1 nkhani