Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 29:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi kuwerenga kwace kwa nsembe zopsereza unabwera nazo msonkhanowo ndiko ng'ombe makumi asanu ndi awiri, nkhosa zamphongo zana limodzi, ndi ana a nkhosa mazana awiri; zonsezi nza nsembe yopsereza ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29

Onani 2 Mbiri 29:32 nkhani