Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 29:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi ansembewo anawapha, nacita nsembe yaucimo ndi mwazi wao pa guwa la nsembe, kucita cotetezera Aisrayeli onse; pakuti mfumu idauza kuti nsembe yopsereza ndi nsembe yaucimo zikhale za Aisrayeli onse.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29

Onani 2 Mbiri 29:24 nkhani