Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 28:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma panali mneneri wa Yehova pomwepo, dzina lace Odedi; naturuka iye kukomana nayo nkhondo ikudzayo ku Samariya, nanena nao, Taonani, popeza Yehova Mulungu wa makolo anu anakwiya ndi Yuda, anawapereka m'dzanja lanu, nimunawapha ndi kupsa mtima kofikira kumwamba.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 28

Onani 2 Mbiri 28:9 nkhani